nyu-ml-nyungwe_luk_text_reg/22/56.txt

1 line
342 B
Plaintext

\v 56 Nyabasa winango wachikazi adamuona atakhala pakutoyewa na motoyo achimunyang'anisisa mkuti, '' Mwamuna uyu pomwe akhana iye.'' \v 57 Soma Petulo adagaza, kuti, ''Mkaziwe, ndikumudziwa lini.'' \v 58 Patapita kanthawe pang'ono winango pomwe adamuona, achiti, '' Ndiwe poomwe m'bodzi wa iwo, ''Soma Petulo adati, ''Mamunawe, ndinelini..''