\v 41 Iye adayenda pakatali na iwo kuti kuthusa mwala ungafike, achikagodama mkupemphera, \v 42 kuti, ''Mbuya, penu mukufuna, chosani mkombo uyu kuna ine. Sikuti kufuna kwangu, soma kufuna kwanu kuchitike.''