\v 5 Khwawa lirirense limdzanyalaziwa, apo phiri lirirense limdzanyalaziwa, apo miseu yakugonyoka ichidzathamuliwa, \v 6 apo minomfu yensene imdzaona chipulumuso cha Mulungu.''