nyu-ml-nyungwe_luk_text_reg/22/69.txt

1 line
328 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 69 Soma kuchokera tsapano mpakana mtsogolo, Mwana wa Munthu amdzakhala kuboko la madidi la mphamvu ya Mulungu.'' \v 70 Wensene adati, ''Ndiye kuti ndiwedi Mwana wa Mulungu?'' Yesu adati kuna iwo, ''Mwaterepoyo ndimwe.'' \v 71 Iwo adati, ''Thangweranyi tikufuna pomwe mboni? Pamene tabva kale tekha kuchokera pakamwa pache.''