\v 14 Yesu adagumana kamphulu kabulu achikapakira popo; ninga kudanembewira, \v 15 "Nampodi kugopa, mkazi waku Ziyoni; ona, Mfumu yako ikubwera, itakhala pa kamphulu ka bulu."