\v 44 Yesu adakuwa achiti, "Iye wakukhulupirira ine, sikuti wakhulupirira ine ndekha soma wakhulupirira pomwe ndiye adandituma, \v 45 apo iye wakuona ine waona iye omwe adandituma.