nyu-ml-nyungwe_jhn_text_reg/01/49.txt

1 line
377 B
Plaintext
Raw Normal View History

2024-03-18 12:42:58 +00:00
\v 49 Natanieli adatawira, "Rabbi, ndimwe Mwana wa Mulungu! Ndimwe Mfumu ya Isaraeli!" \v 50 Yesu adatawira achiti kuna iye, "Thangwera ndakuuza, 'Ndidakuona patsinde pamuti wamkuyu,' wakhulupiriratu? Uniona bzikulu kuposa ichi." \v 51 Kinangoka iye adati, "Indetu, indetu, ndikulewa kuna iwe, umdzaona kudzaulu kutafunguka, apo anjero wa Mulungu akubuluka pa Mwana wa Munthu."