nyu-ml-nyungwe_heb_text_reg/10/38.txt

1 line
301 B
Plaintext

\v 38 Soma wakulungama wanguyo amdzakhala na moyo wakuchokera mchikhulupiriro. Penu anibwerera mmambuyo, moyo wangu unidekedwa lini naye. \v 39 Soma ndife lini wina wa wale omwe abwerera mmambuyo kuchitayiko, soma ndife wina wa wale wakukhala nacho chikhulupiriro cha ku chipulumuso cha miyoyo yawo.