\v 13 Khalani wakudikila , imani mwa changu m'chi \p khulupiliro, chitani ninga amuna, khalani wamphamvu. \v 14 Bvumani kuti bzense mun'chita imwe bzichitike muchikondi.